Topsongs van Onesimus
Vergelijkbare songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Onesimus
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Armstrong Kalua
Songwriter
Richard Ndasowa
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
Savage
Producer
Songteksten
Tell me what's the problem baby
M'mose ndayambila kudikila
M'mpaka dzuwa lalowa
Ineyo kudikila, mwina ubwela
Maso chewu chewu kunjira
Maybe utulukila, mwina ubwela
Dzulo unati mawa
Dzana unati mawa
Nanga lero bwanji
Tell me what's the problem baby
Dzulo unati mawa
Dzana unati mawa
Nanga lero bwanji
Tell me what's the problem baby
Kodi ubwela iwe, Kodi ufikadi
Ndiyakhule, ndiyakhule
Kodi ubwela iwe, koma Ngati wasitha, pulani
Ndimasule, undimasule
I've been waiting, waiting
I've been waiting, waiting, for you
Kudikila nkowawa
I've been waiting, waiting
I've been waiting, waiting, for you
Kudikila nkowawa
Kapena matola afela panjira
Kapena bus break down
Nkhawa ya ndigwila
Phone yako sikugwila
Kapena wakumana ndi dolo wina
Wakunyengeze babe mwina wakuwina
Wakunamiza sindingakusamale mwina
Tell me what's going on oh
Dzulo unati mawa
Dzana unati mawa
Nanga lero bwanji
Tell me what's the problem babe
Dzulo unati mawa
Dzana unati mawa
Nanga lero bwanji
Tell me what's the problem babe
Kodi ubwela iwe, Kodi ufikadi
Ndiyakhule, ndiyakhule
Kodi ubwela iwe, koma Ngati wasitha, pulani
Ndimasule, undimasule
I've been waiting, waiting
I've been waiting, waiting, for you
Kudikila nkowawa
I've been waiting, waiting
I've been waiting, waiting, for you
Kudikila nkowawa
Lyrics powered by www.musixmatch.com