Tekst Utworu

Ayeyeye, yeah Ukayatsa Tv tili po, pompo Ndi ma bo, bobo Ma show tili mo, momo Zili cho, choncho Kuyiworker aicho, chocho Za mago, gobo Kukometsa ngati so, sobo tili bho, bhobho Za ukape ine no, nono Koma udo, dolo Kulikonse tili ko, konko Tikuyenda ngati so, soso Yatsa TV tili po, pompo Ndi ma bo, bobo Ma show tili mo, momo Zili cho, choncho Ukatipeza tili konko, Ay ye, aye ukatipeza tili Konkoo iwe ukatipeza tili mo, momo Ndi ma bobo Sitikola ngati coco Zili bho bhobho Zauzoba ife to toto Koma ubo Bosso Gassed up ngati To, Total Tikudripa ngati do, dontho Achina eish, Nde ifeyo! Timayiphula ndiwozo zili ifeyo Afana aubiggie nde ineyo Ka phinifolo ka ufumu sinanga ma Kingpin a Kadigo, gong'o Za ma ko, kono Nafika kale ngati ago, gogo Managing ngati Ngo, ngongo Yatsa TV tili po, pompo Ndi ma bo, bobo Ma show tili mo, momo Zili cho, choncho Ukatipeza tili konko Ay ye, aye, ukatipeza tili konkoo iwe Ukayasa TV tili po pompo Ndi ma bo bobo Ma show tili mo momo Zili cho choncho Ukatipeza tili konko, Ay ye, aye, ukatipeza tili Konkoo iwe Ukatipeza tili mo Tili konko, tili konko, tili konko
Writer(s): Afana Ceez Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out