Vídeo da música

Zonse Nzabwino
Assista ao videoclipe da música {trackName} de {artistName}

Créditos

PERFORMING ARTISTS
Sir Paul Banda
Sir Paul Banda
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Sir Paul Banda
Sir Paul Banda
Composer
Lucius Banda
Lucius Banda
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
Sir Paul Banda
Sir Paul Banda
Producer

Letra

Mulungu adalenga munthu Ndi zonse zosangalatsa kale Malemba ati anawona Kuti zonse zinali bwino ndithu Anamupatsa munthu mawu Kuti choncho asangalale ndi kumuimbila Analidalitsa banja Ndicho chinthu choyeletsedwa pamaso pake Koma nthawi zina timalephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Ambiri tili kulephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Anthu achiwelewele Amapita ku dance ndi zolinga zoyipa Wena kovina komweko Amakadalitsidwa ndi uthenga wabwino Zokondwetsa mukuwona lero Ndi chifukwa chamaphunziro akusukulu Wena sukulu yomweyo Amasanduka nayo mkango kumapha wanthu Nthawi zina timalephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Ambiri tili kulephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimaoneka ngati zoyipa Bambo wa nkhanza sapeleka Njoka kwa mwana wake m'malo mwa nsomba Koma mwana akapupuluma Minga yomweyo yansomba ingamuphe Ndi udindo wa achinyamata Kukometsa dziko la pansi likhale lokoma Popeza zonse zolengedwa Mulungu anaziwona kuti nzabwino Koma nthawi zina timalephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Ambiri tili kulephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Nthawi zina timalephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Ambiri tili kulephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Nthawi zina timalephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Ambiri tili kulephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi Ndipo izo zimawoneka ngati zoyipa Koma nthawi zina timalephera Kugwiritsa ntchito zinthuzi
Writer(s): Sir Paul Banda Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out