Lyrics

Niziba choneka monga kwe ninayenda Ati nina kuibalako wewo mwamene bambili bamachita Awe kuja kubazungu bananimanga Mulundu wene sininachite newo, oh Muja muchofungo, maganizo yanga siyanakusiye yai Kulibe iwe mu m'tima sebe sinasavaive Ine muja nenzo lota chabe mukhazi wanga Mukhazi wanga Chioneka monga makalata nenzo lemba siyanakupeze Yanasobela pa ndeke Elo futi sinikublema poganiza ati ninakutaba Ine nabwelo kutenga lelo Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true Uyu ninamuvomela chabe ndaba ine sinenzepo Ndine nili na m'tima wako Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true Uyu anakuchankwila chabe unaona monga ninakusiya But lelo nabwela aah-ah Nichikonko chamene chanileta kuno Nikuyewa life twenze nayo Peninafika ninanvela ati ukwatiliwa pa Sondo Sina plane nobwelako, m'tima ndiye wanileta kuno Siningaleka akukwatile ngati ukali unikonda Ndine nikuziba mushe, naiwe uniziba bwino Pe nenzo yenda chifukwa nachiziba, ah Ine ninayenda kuma punzilo kuti iwe naine tinkankale bwino nika bwela Chioneka monga makalata nenzo lemba siyanakupeze Yanasobela pa ndeke Elo futi sinikublema poganiza ati ninakutaba Ine nabwelo kutenga lelo Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true Uyu ninamuvomela chabe ndaba ine sinenzepo Ndine nili na m'tima wako Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true Uyu anakuchankwila chabe unaona monga nakusiya But lelo nabwela aah-ah Zizimila sakila ma picture muma ganizo uni uze Bushe ona chani uka ona iwe naine? Ngati waya zonda ngati chikondi changa sichina kukondwelese iwe Nizayambambo sinizambwelapo futi newo Zizimila sakila ma picture muma ganizo uni uze Bushe ona chani uka ona iwe naine? Ngati waya zonda ngati chikondi changa sichina kukondwelese iwe Nizakusiya nizayenda Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true Uyu ninamuvomela chabe ndaba ine sinenzepo Ndine nili na m'tima wako Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true Uyu anakuchankwila chabe unaona monga nakusiya But lelo nabwela aah-ah Don't say you do Don't say you love him too Don't say you wanna spend the rest of your life with him 'Cause it's not true
Writer(s): Robert Banda Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out