Lyrics

Oh, (Ritaa.Piksy) eh Eh. Eeee hey Ukundiiwala, nde chikondi chikuwawa (you're forgetting me, so the love is hurting) Chikondi chikuwawa (the love is hurting) Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala, nde mtima ukuwawa (you're forgetting me, so my heart is aching) Mtima ukuwawa. (My heart is aching) Mtima ukuwawa. Eh (my heart is aching) Kunjaku kwacha, tili pompaja (Its dawn, and we're still here) Milandu yanji yosatha? Oh oh oh (Endless fights, oh oh oh) Unasiya kunditchula (You stopped calling me) Timaina tachikondi tija (Those sweet sweet names) Kodi waponda mwala? (Have you found another?) Zoti uli ndi mkazi pano waiwala (That you have a woman, you seem to forget) Sumandilabadila, mwina Wapeza wina (You don't care, maybe you've found another) Ndayamba kukaikila, kuti udzandisiya (I am scared, that you will leave me) Mtima ukuwawa (My heart is aching) Mtima ukuwawa (My heart is aching) Zikundivuta ndafuna kumvetsetsa (I am trying to understand) Koma ndalephera (but I am failing to) Ukundiiwala nde Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala nde mtima ukuwawa Mtima ukuwawa Mtima ukuwawa. Eh I've been stressed lately, work mainly Zonse Zili bho, Chikondi still stately I appreciate that you respect me Chikondi chiyambiranso being tasty I am sorry I let you down Every week am out of town Babe I'm working, but thanks for checking Ndipanga zotheka kuti zonse zitheke (I will do my best to make it right) I am the luckiest man in the world Ndi iwe pambalipa (With you by my side) I can never fail Ndiwe mkazi Wakumwamba I can tell Nde usamadandaule (So don't you worry) you're my girl Ukundiiwala nde, Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala nde, mtima ukuwawa Mtima ukuwawa, mtima ukuwawa. Eh Ndili ndi mantha, (I am afraid) Ndingadzagende Katauluka. (I might stone after it has flown away) Oh no, oh no... Ndiwe wekha,sukubetsa (It's only you,) Umabebetsa sakugwetsa (You spice it up, they can't take you down) Akulenga, sakuvencha (They are nothing) Ndine chips, iwe ndiiwe Ketchup (I'm the chips, you are the Ketchup Ukundiiwala, nde chikondi chikuwawa (You're forgetting me, so the love is hurting) Chikondi chikuwawa (The love is hurting) Chikondi chikuwawa. Eh Ukundiiwala, nde mtima ukuwawa (You're forgetting me, so my heart is aching) Mtima ukuwawa. (My heart is aching) Mtima ukuwawa. Eh (my heart is aching)
Writer(s): Rita Kalonga Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out