Music Video

Music Video

Credits

PERFORMING ARTISTS
Simon Chimbetu & Orchestra Dendera Kings
Simon Chimbetu & Orchestra Dendera Kings
Performer
Simon Chimbetu
Simon Chimbetu
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Simon Chimbetu
Simon Chimbetu
Composer

Lyrics

Chauta woo!
Tsiku loyamba lomwelija
Lomwelija
Limene munali lulenga ine
Ndilomwelo
Ndilomwelo ndikuti beta munakanchinja nkhope
Chauta woo!
Tsiku loyamba lomwelija
Lomwelija
Limene munali kulenga ine
Ndilomwelo
Ndilomwelo ndikuti beta munakanchinja nkhope
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliulira
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliupita or bwera
Silidziwika bwino
Ikoma munakanchinja nkhope
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliulira
Nkhope yanga
Ndikhala ngati ndiliupita or bwera
Silidziwika bwino
Ikoma munakanchinja nkhope
Oyang'ana
Andiyesa Chitsilu yawa
Oyang'ana
Andiyesa wakuba ine
Oyang'ana
Andiyesa wolodza
Chauta munakanchinja nkhope
Oyang'ana
Andiyesa chitsilu ine
Oyang'ana
Andiyesa wakuba ine
Oyang'ana
Andiyesa wolodza
Chauta ndaona bvuto
Chauta woo!
Tsiku loyamba lomwelija
Lomwelija
Limene munali lulenga ine
Ndilomwelo
Ndilomwelo ndikuti beta munakanchinja nkhope
Chauta woo!
Tsiku loyamba lomwelija
Lomwelija
Limene munali kulenga ine
Ndilomwelo
Ndilomwelo ndikuti beta munakanchinja nkhope
Oyang'ana
Andiyesa Chitsilu yawa
Oyang'ana
Andiyesa wakuba ine
Oyang'ana
Andiyesa wolodza
Koma munakanchinja nkhope
Oyang'ana
Andiyesa chitsilu ine
Oyang'ana
Andiyesa wakuba ine
Oyang'ana
Andiyesa wolodza
Chauta ndaona bvuto
Dendera Kings
Yes!
Dendera Kings
Written by: Simon Chimbetu
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...