Lyrics

Zoti kunja kuwala Palibe angatsutse Kuwona madzi mu khwawa oooh Palibe angafunse Kunja kuwala yeay yeah Palibe angatsutse Kuwona madzi mu khwawa oooh Palibe angafunse Ndendende ndi mmene The way that I feel for you Palibe chimene I wouldn't do for you Zoti ndimakukonda Sizovuta kuwona Chikondi changa pa iwe ndichokuya Ndendende Zambezi Awh yeah Ndendende Zambezi Ooohhhh Ndendende Zambezi Ayayayayaya ohhh Ndendende Zambezi Ayayayayaya oohhh Dzuwa saalozelana Zamumtima saauzilana Koma zoti ine ndimakukonda iwe wekha Palibe angatsutse See my actions revealing The way that I'm feeling Na chikondi chokhachi palibepo oleletsa Ndendende ndi mmene The way that I feel for you Palibe chimene I wouldn't do for you Zoti ndimakukonda Sizovuta kuwona Chikondi changa pa iwe ndichokuya Ndendende Zambezi Awh yeah Ndendende Zambezi Ooohhhh Ndendende Zambezi Ayayayayaya ohhh Ndendende Zambezi Ayayayayaya oohhh Zoti ndimakukonda Sizovuta kuwona Chikondi changa pa iwe ndi chokuya Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah Ndendende Zambezi Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah Ah yeah yeah yeah yeah yeah yeah Ndendende Zambezi
Writer(s): Theresa Phondo Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out