album cover
Zonsezi
276
Hip-Hop/Rap
Zonsezi was released on July 1, 2021 by KC VISUAL as a part of the album Zonsezi - Single
album cover
Release DateJuly 1, 2021
LabelKC VISUAL
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM70

Credits

COMPOSITION & LYRICS
lovemore majuta
lovemore majuta
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Braxxy
Braxxy
Producer

Lyrics

Yah
Ya achina Seven adah
Ambuye amatikonda (Yah)
Mulungu amatikonda (Yah)
Chauta amatikonda (Yah)
Ambuye amatikonda (Yah)
Amatidzutsa tikagwa
Amatichilitsa tikadwala
Timuyimbile kuti izi-pitilile
Ambuye amakonda aliyense
Mphepo imapeza aliyense
Mvula imagwera denga la aliyense
Dzuwa limapeza aliyense (Yah)
Onani munthu, onani mbuzi, onani nkhuku, mwanapiye, khwiyo
Onani dzuwa, onani mwezi, chiphariwari khakhakhakhakha
Analenga zonsezi (Yah)
Analenga nyanjazi (Yah)
Analenga nyamazi (Yah)
Analenga chambachi (Yah)
Ngakhale mdima ungakure bwanji padziko lapansi kunja kumachabe
Ngakhale mvula ingavumbe bwanji padziko lapansi nyerere sizifa
Analenga manyazi (Yah)
Analenga nsanjezi (Yah)
Analenga nkhawazi (Yah)
Analenga imfayi (Yah)
Analenga chisoni (Yah)
Analenga misozi (Yah)
Analenga chikondi (Yah)
Analenga mtendere (Yah)
Analenga satana (Yah)
Anthu m'matsapana (Yah)
Anthu m'mangophana (Yah)
Ana ajaja wa (Phrr)
Ambuye amatikonda (Yah)
Mulungu amatikonda (Yah)
Chauta amatikonda (Yah)
Ambuye amatikonda (Yah)
Amatidzutsa tikagwa (Yeah-yeah)
Amatichilitsa tikadwala (Yah-yah)
Timuyimbile kuti izi-pitilile
Yah, yah, yah, yay, yah, yah, yah, yah
Yah-yah, yah-yah, yah-yah, yah-yah
Chopangidwa padziko lapansi, chimathela pa dziko lapansi
Nkango Wayuda sangalore, mpaka tsiku lina tizayimba--
Mtendere (Yah), mtendere (Yah), padziko lapansi (Yah)
Yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere (Oh my God, oh my God, oh my God)
Mtendere (Yah), mtendere (Yah), padziko lapansi (Yah-yah)
Yesu ndi mfumu yathu, ndi mfumu ya mtendere, eh (Oh my God, oh my God)
(Yah, yah)
Written by: lovemore majuta
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...