Lyrics

Kale ndili mwana ndisanazitolele Mabvuto anga anali lamba wa adadi Ndinkafunitsitsa kukhala pandekha Poti amama samalola kuyenda ndi usiku Lero ndakula nyumba ndapeza Koma chondidabwitsa ndifuna nditakhala mwana Mabvuto achuluka ntchito kusowa Koma rent angokweza ambuye ndipangeni mwana Oh mwana Eh mwana Ah mwana Ndipangeni mwana Oh mwana Eh mwana Ah mwana Ndipangeni mwana Kale tili wana ife tinkasonkhelana Zinthu zikavuta tinkathandizana Azibale nawo ankatiwona daily poti zinthu zinkayenda Lero ndakula moyo kulimba Mmalo mondithandiza amandi gulila mowa Mabvuto achuluka ntchito kusowa Koma rent angokweza ambuye ndipangeni mwana Oh mwana Eh mwana Ah mwana Ndipangeni mwana Oh mwana Eh mwana Ah mwana Ndipangeni mwana Oh mwana Eh mwana Ah mwana Ndipangeni mwana Oh mwana Eh mwana Ah mwana Ndipangeni mwana
Writer(s): Teddy Maliza Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out