album cover
Holiday
91
Hip-Hop/Rap
Holiday was released on February 4, 2022 by 3767216 Records DK as a part of the album Le$$On$
album cover
AlbumLe$$On$
Release DateFebruary 4, 2022
Label3767216 Records DK
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM97

Music Video

Music Video

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Evans Chimwala
Evans Chimwala
Songwriter

Lyrics

Chinali chaka cha 2020
Chaka cha minyama, cha midwedwe
Chaka cha holiday, chaka cha maluzi heavy
Chaka chomwe ndinaspenda dollar yonse sindinaseve
Ndi chaka tinalemeletsa company ya Ve-ve
Lero moyo, mawa kufa
Mu nthawiyi ndinali chabe yuthi wa mu two fa
Geli tinangotsekela semester isanathe
Aliyense kwao chimfine chisamugathe
Vuto lake nafe sitinkazisata
Maluzi, tinkangodalira ka free data
Olo news, za current affairs sitinkatha
Bola kumvera Martse; too ghetto too gutter
Ma cruiser za boma kulengeza paliponse
Chonde Sambani manja mwanu nthawi zonse.
Ya mask imasowa, pena ngati ndingotola
Kuganizila ubwino wa mask ndi wa Bhola
Mu ghetto mwathu zingini zinasintha kwabasi
Abusa kupatsana nawo moni wama rasi
Aliyense mu church mask ngati ma Ninja
Anthu anadziwa kufunikila kwa ginger
Anthu tinadzola zinthu mu 2020.
Pa shop iliyonse No mask, No entry
Ma bigiri ndi sopo pambali on every corner
Holiday ya 2020 inali ya CORONA
Written by: Evans Chimwala
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...