album cover
Anana
album cover
Anana was released on June 17, 2022 by 2071927 Records DK as a part of the album Mtunda
AlbumMtunda
June 17, 2022
Label2071927 Records DK
LanguageEnglish
BPM89
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Yo Foxy
Chi Piksy chimfana chodziwika ndi boma
Zinayamba mwachibwana
Ti ma show pa Gymkhana
Ife tilibe chikwama
Enawa ankatikana
Kukwiya tikasanja
Kumaseka tikanjanja
Osalakwa kutilanga
Kutiyang'anira under
Kufeela ngati mlendo
Kukhala ngati zoba opanda Frenzo
Koma ndi chi hope kugwira ntchito
Anawapanga mavuto onse history
Ndeno
Zikatere itsanana
Tere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Tere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Pano tiri ku mtunda
Tikumatha kumajambura video kunja
Zomwe sitikadyazo tikudya
Sitiyenda pansi nde tili ndi nyumba
Kale ankadutsa nkupita osatipatsa Moni
Kuyimba osayankha phone
Podutsa ma Ninja kuyika stones
Pena ngati ungopita Joni
Lero holiday(Namibia)
Pop that champagne again(waziziwa)
Sikuti nkufuna kunena kuti wandilira
Uwu ndi umboni wanga mphwanga ndinashuphika
Ndeno
Zikatere itsanana
Tere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Tere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Uuuh
Thank God for life
Thank God for everything
'Cause paliponse pamene you are
Aliponso wina wake amapafuna
Hoooh
Thank God for life
Thank God for everything
Cause paliponse pamene you are
Aliponso wina wake amapafuna
Tsono
Zikatere itsanana
Tere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Tere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Zikatere itsanana
Tere itsanananana
Zikatere itsanana
Written by: Evans Piksy Zangazanga
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...