album cover
Tiye
111
World
Tiye was released on February 16, 2018 by Zembani Music Company as a part of the album Crimes
album cover
AlbumCrimes
Release DateFebruary 16, 2018
LabelZembani Music Company
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM103

Credits

Lyrics

Mmmh mmh
Ay yah yah yah!
Dzaka seven dzapita
Tikukhalira limodzi
Chikondi chathu chikukula
Ndafuna ndimange woyera
Tsiku loyamba kukuona
M'dangoti kakasi
Ndati Jehovah wagwetsa angel
Kuti ndipeze mkazi
Tiye Iwe (tiye)
Kwacha Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye) Iwe
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Kwacha tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tikakumbuka kuchawe
Ulendo kutsatira
Ndikamuone kwacha
Tikamange woyera
Suit yanga ndavara
Dress yako wavala
Makolo akonzeka
Tikamange woyera
Ndimakumbuka mtatenga phone
Yako ya m'manja
Kunamizira kusilira uku ndikuba nambala
Ndinanenadi motsindika
Ndiwe mayi malanga
Lero ka liza ndizande
Ndi ana anthu kwacha
Tiye, kwacha Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye) Iwe
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Kwacha tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tikakumbuka kuchawe
Ulendo kutsatira
Ndikamuone kwacha
Tikamange woyera
Suit yanga ndavara
Dress yako wavala
Makolo akonzeka
Tikamange woyera
Eeeh eeh, aha aha
Oh whoa
Tatiye, tatiye, tatiye
Mmh tiye Iwe (tiye)
Kwacha Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Kwacha Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tikakumbuka kuchawe
Ineyo kutsatira
Ndikamuone kwacha wanga
Tikamange woyera
Suit yanga ndavara
Dress yako wavala
Makolo ali akonzeka
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Kwacha Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tikakumbuka kuchawe
Ulendo kutsatira
Ndikamuone kwacha wanga
Tikamange woyera
Suit yanga ndavara
Dress yako wavala
Makolo ali akonzeka
Tikamange woyera
Suit yanga ndavara
Dress yako wavala
Makolo ali akonzeka
Tikamange woyera
Suit yanga ndavara
Dress yako wavala
Makolo ali akonzeka
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Kwacha Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tiye Iwe (tiye)
Tikamange woyera
Written by: Lucius Banda
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...