album cover
Mukamutule
8
World
Mukamutule was released on July 29, 2016 by Media 360 as a part of the album Ceasefire
album cover
Release DateJuly 29, 2016
LabelMedia 360
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM90

Credits

Lyrics

Oooh ooh
Achimwene njira yonse munayenda anthu awiri
Achimwene bola mukawatule
Mwaona atsikana achizulu awa ndiwala
Achimwene bola mukawatule
Chikondi chanu chakwangochokoma pokwera
Achimwene bola mukawatule
Mkazi akhalire kunyozedwa muno mu town
Achimwene bola mukamutule
Kwa amayi chonde mukamutule
Kwa amake koti akhale moyo
Aferanji chonde mukamutule
Kwa amake koti akhale moyo
Aferanji
Takumbukani mwambo uja makolo adapereka
Nyumba muja muli chiwelamire
"Mukayendela mdzengo musati asakhwi afumbula"
Achimwene bola mukawatule
Mkazi akhalire kunyozedwa muno mu town
Achimwene banja samatero
Khala pansi muganize komwe inu muchokera
Achimwene kunja kwawawasa
Kwa amake chonde mukamutule
Kwa amake koti akhale moyo
Aferanji chonde mukamutule
Kwa amake koti akhale moyo
Aferanji
Written by: Lucius Banda, RR
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...