Lyrics

Ngati nyumba samanga Yehova Oyimangayo amanga chabe Ngati banja samanga Yehova Oyimangayo amanga chabe Ndinveleni Yehova Ndalila misonzi ndikutopa Ndinveleni Yehova Ndalila misonzi ndikutopa ine Nthawi yozemba inatha Pano ndabwela Ndabwela ndi nsembe yopseleza Ndikupemphela Mukhululuke machimo anga Mundilandile Ndinali ine nkhosa yosochela Ndazindikila Ngati nyumba samanga Yehova Oyimangayo amanga chabe Ngati banja samanga Yehova Oyimangayo amanga chabe Ndinveleni Yehova Ndalila misonzi ndikutopa Ndinveleni Yehova Ndalila misonzi ndikutopa ine Msambizgi wane Dada wane Ndazomelezga vya kukhumba vyinu Chitani umo mwakhumbira Pakuti moyo opanda inu ulichabe Ndazindikila ine Nzeru zanga Mphanvu zanga Mukayikapo dzanja Zimakhala in abundance Mbuye palibe chomwe ndingakwanitse ine opanda inu Palibe Ngati nyumba samanga Yehova Oyimangayo amanga chabe Ngati banja samanga Yehova Oyimangayo amanga chabe Ndinveleni Yehova Ndalila misonzi ndikutopa Ndinveleni Yehova Ndalila misonzi ndikutopa ine Mundinvele ine Yehova Mundinvele ine Yehova Mundinvele ine Yehova Mundinvele ine Yehova
Writer(s): Teddy Maliza Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out