Music Video
Top Songs By Mellz Kumpanje
Credits
COMPOSITION & LYRICS
Mellanie Mellz Msumba
Songwriter
Lyrics
Woooo
Hahaha
Sisonke neh
Lero nde tiuchapatu eeeh
Iwe Wani Sauzande yonseyo ndimwere mowa ine
Mphwanga maluzi samakuchapa dollar yonseyo ndingabande
Mwezi wachikhalire Bhola
M'mene ikutchipila mu bangwe
Kwa hiki kwa chichi Rasta Mellz Kumpanje
Ma husha Sha sha alabwe ma husha
Tidya koma mochedwa hah
Tidyera ngosha lero sitikulora bona ma Sosha
Mabebeza kundipeza akufuna ma Sosha
Timweseni castle
Ngati Ali Fili handede Tenga
Dollar sitikutola tikuvuulira mchenga
Nip imodzi ujibe nawo aah iwe tchenga tchenga
Olo zindipweteka ine ndilipira ndekha
Ulibe money Eti
Wabwera dala cholinga tizikangana Eti
Botolo mwan'nyamula?mulibe kanthu Eti
Tiziti ndinu mabwana mwagwera mu fridge tchubu Eti
Kudabwa mwa'nlubwa
Biggy tengani hunters uyu
Aaah iwe fanta chani
Ganja palibetu apa
Aaah iwe chamba chani
Kwabwera ma husha
Nde ukuwasiya panja
Abwere alowe chifukwa
Tikufuna zipweteko
Pweteko pweteko pweteko zipweteko
Pweteko pweteko
Tikufuna zipweteko
Pweteko pweteko pweteko
Zipweteko
Pweteko pweteko pweteko
Yomweyo galu iweeee
Writer(s): Mellanie Msumba
Lyrics powered by www.musixmatch.com