album cover
Karma
1,725
Hip-Hop/Rap
Karma was released on August 14, 2023 by KINGPIN as a part of the album Phinifolo Yaufumu
album cover
Release DateAugust 14, 2023
LabelKINGPIN
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM99

Music Video

Music Video

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Paul Chisiano
Paul Chisiano
Songwriter

Lyrics

Ooooh, mmmmhhh
Mmh Sunkati ndinali kale
Lero wandifuna iwe galu eti
Zikupeta unkati mphale
Lero tikudya iwe usale
Ngongole unkati sunday, monday kenako
Usandipatse
Pano ndikuchakacha nde uzindipempha iwe ndi bakha eti
Ndinjoye nane
Ndiyibakisheleko nane
Ndikutapa ngati wa ndale Hi Ho
Zi ma ho ngati Vicky Marley
Iwe Sungayimake
Size singakukwane
Unayiphwekesa kale mpake sukutukuka nawo m'bale
Ndinakuuza kale
Karma izakutsata
Karma izakutsata
Karma izakutsata
Karma izakutsata
Zoma eh khomelelana ndi za chimwana
Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka
Zoma eh khomelelana ndi za chimwana
Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka
Nditakufusila unandikana
Lero (hey baby), iwe gwape eti (aaah)
Iwe ndikatchula honey
Imakhala money, mukawuzane
Amanditcha bwana KingPin (Shasha)
Ndimacheza ndi ma ding ding ding
Ndikumveka ngati ringing
Nde uzindifuna are you kidding me? ah
Sungayimake
Size singakukwane
Unayiphwekesa kale mpake sukutukuka nawo m'bale
Ndinakuuza kale
Karma izakutsata
Karma izakutsata
Karma izakutsata
Karma izakutsata
Zoma eh khomelelana ndi za chimwana
Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka
Zoma eh khomelelana ndi za chimwana
Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka
Written by: Paul Chisiano
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...