Listen to MWANTINTI (feat. Teddy Makadi & Pon G) by Phyzix

MWANTINTI (feat. Teddy Makadi & Pon G)

Phyzix

World

4,616 Shazams

Lyrics

Yeah It's Only Entertainment Wole Wala Yeah Very Good Very Good Kukukisa pang'ono ngati ka 2par Unati ndisamasuke kwanu ndi koshupha Ndikafika pa gate n'salize hooter Ndizingolemba message mpanda uziwudumpha Pena pake ndiwe ka mkazi kofuntha Zomwe tikupangazi akwanu azandikuntha Alibe nazo zoti ndine wotchuka Zoti ndimaoneka pa TV pa Luntha Ndi ka light skin girl ngati Amarula Body lining sanayuze ruler Love language yake nnati dollar Ine mayine koma sindilola Let me take you to Munalula You rob my heart ndiwe kawalala Mmangofuna uzisangalala Ma love obhebha ngati za mankhwala Mmh love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Zikukoma ngati nyama yakufupa Battery la moyo wanga lafika pa full bar Koma kwanu ati ndine kape ndine luga Amandionera diso limodzi la Ruger I'm gonna represent you though I ain't passed the bar Baby girl I gotchu we gonna go far Ngati Bluetooth devices tinalinka Mami ndinu chida ndinu kilinka Sumasunga tu ma secret mayine secret Zimandiwaza zopita ku ma picnic Tiye kunyanja ndikayiphula ticket Na iwe ndi ndi ndikumata ti Ati Chikondi ndi mbo Kondi ndi mbola Kwa iyeyo bola ndimpatse zi dollar Komabe ine love yako nde ndiyitola Strictly lobola ndiyomwe uyiwona Mmh love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Uzipola moto ukamandithoka Uchepetse za mavuvu siwe motorcar Zomwe ndimafuna utsanzike pochoka Nsanje zayamba kuchuluka mtima utchoka Ndisaone kakape ka kukuthoka Sindisekelera kakaka zopotoka Ukafuna dollar trans ID kuti kha Usamaope kupititsidwa ku chatinkha Mkaziyu ndi wanga wa ine ndekha Sitimaitana gulu potenga chindekha Ndikati ndikugwa amandiwakha Uyu nde ndimanyadila kuti ndinasankha Very Good Ndikumva tseketseke ngati sugar (Illovo) Ngati kumaloto (Loto) Hunnie! You're my Princess Kukonda iwe sindipanga regret Mmh love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi) Mmh I love you more (bebi) Mmh I love you mwantinti (bebi)
Writer(s): Noel Phyzix Chikoleka Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out