album cover
Apolisi
267
Hip-Hop/Rap
Apolisi was released on August 25, 2023 by 1740343 Records DK as a part of the album Apolisi - Single
album cover
Release DateAugust 25, 2023
Label1740343 Records DK
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM70

Music Video

Music Video

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Happy Titani Bakolo
Happy Titani Bakolo
Songwriter

Lyrics

Iweee!!!
Apolisi amu Limbe anandigatha
Ngati ku Thyolo, ndinawafunsa kuti ndataa
Ngati suunalakwe bwanji phwanga umathawa
Pepani bwana sichina ayi anali mantha
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Tinali mu Limbe depot timangomenya umodzi umodzi
Ine ndi Fredooo, osadziwa kuti tikathera m'chitokosi
Sinanga neighbor ndati aise tizivayira limodzi
Kenaka nkhani inanso nkhani ngati page ya Mikozi
Tikuvaya Chigumula, tati tikakwere ku Petroda kwa Kapenga
Poti sitinalakwe apolisiwa tisachite kuwazemba
Kudutsa mwakachetechete, anafunsa mukuvaya kuti mamemba
Ine ndimantha nnayamba mmmhu nnayamba kudaka nnayamba kucheka
Ndikudya chi turn andifaka chi stonzi
Ndati nditele ndili mu dothi
Unali kuti ine, misozi, dzina ndi ndani ine, misozi
Akuti ndawang'ambira jombo, ndati mayo ndaputa ngozi
Siine wakuba bwana n'nali mu depot ndimamenya dzima shot komaa
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Apolisi ndi abale athu
Anatitengera mkati ndinkangoona chimdima
Mmene timafika pansi ndinatuluka ndikutsimphina
I didn't have a flu koma tsiku ilili ndinachimina
I didn't have a flu koma tsiku ilili ndinachimina
Dzina n'ndani? ndati Happy
Abwana chonde musanditape
Dzina iwe? Bakolo Happy
Kakwana kuti ndichilape
Before they booked me, n'namva phone yanga ikulira
Anati yankha phwanga chimenecho tikuzimitsira
"Yes Baxxy" ndati zabwino? zabho aise?
Akuti "bwanji ukumveka sad you sound too low aise"
Ndili ku Limbe police, panopa mmmhhh ndikulowa aise
Ukunena zoona? chonena panopa chikundisowa aise
KOMAAAA!
Written by: Happy Titani Bakolo
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...