album cover
Ndiwe
album cover
Ndiwe was released on September 27, 2023 by Independent as a part of the album Ndiwe - Single
September 27, 2023
LabelIndependent
BPM99
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

(Ndiwe?)
Ndikaona Maso mwako
Mtimwa wanga umasisima
Makamaka ukangondilankhula
Moyelekeza ndimamva kukoma aah
Ndapata Ndapata Ndapata ine eeeh
Ndadala ndadala ndadala ine
//Ndimagwitsa tsemwe ine ndikuona
Ndinagwira iwe ine mwali zoona..
Chorus
Kodi ndiwe ?Amene ndinkafuna
Kapena ndiwe? Olonjezedwa uja aah
Ndidikile? Kapena ndikhazikike
Mudziko lachikondi/lachikondi iih
Verse2
Anzanga akuti ndiwe okongoletsa
Anthu achuma mabwanawa azindilanda
Ena akuti patalike pangafupike
uzandithawa!! uzapeza wina
Koma baby iyee mutima
Muli mafuso yeh iyeh yeh iye
Kodi ndapata ndapata ndapata ine..
Ndadala ndadala ine eeh..
Chorus
Kodi ndiwe
Amene ndinkafuna
Kapena ndiwe
Olonjezedwa uja aah
Ndidikile?
Kapena ndikhazikike
Mudziko lachikondi lachikondi iih
Written by: Samuel Kaira
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...