Credits

PERFORMING ARTISTS
Praise Umali
Praise Umali
Vocals
Kell Kay
Kell Kay
Performer
Zeze Kingston
Zeze Kingston
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Praise Umali
Praise Umali
Songwriter
Kelly Kambwiri
Kelly Kambwiri
Songwriter
Robert Ching’amba
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Praise Umali
Praise Umali
Producer
Sonyezo
Sonyezo
Producer
Matthew Mphande
Matthew Mphande
Producer

Lyrics

Saw You Once, moving too fast already
Would you meet my daddy?
Can I see your family?
Mtima iwe Puma, Osapuma
And i Told my Mommy, I've found the one
She said "Mwakumana kuti?"
Ku Tiyeni Takumana Ku Tiyeni
Nde tiye baby
Ndine mpaka manda
Girl i know that i love you right
Long as I'm alive
Koma anzanga akudabwa
Why?
How you hold me down?
Nawo Akufunsa anthu Akufunsa
Mukathera kuti?
Ku tiyeni Ankhoswe Tiyeni
Ku tiyeni ku Ukwati Tiyeni
Ku tiyeni tikathera ku Tiyeni
Ku tiyeni ku Ukwati Tiyeni
Ku tiyeni (Ay! yo! Tiyeni!) tikathera ku Tiyeni
(Tiyeni! Tiyeni! Tiyeni! Eish!) ku tiyeni Ku Ukwati Tiyeni
Y'all Ready know
Unandiuza don't rush
Akuti true love never runs out
Ndinakumvera Nkhani zima rumours
Osadziwa mwanakazi nakukhumba khumba
You belong to me
Eko sunga Key
When I'm with you I'm free
You is where i wanna be
You belong to me
Eko sunga Key
When I'm with you I'm free
Koma anthu akudabwa
Ati you hold me down
Anzanga Akufunsa
Nawo Akufunsa
Tikathera Kuti?
Ku Tiyeni Ku Tiyeni
Anthu Akufunsa
Tikathera kuti?
Ku Tiyeni Ku Tiyeni
Ku tiyeni tikathera ku Tiyeni
Ku tiyeni Ku Ukwati Tiyeni
Ku tiyeni tikathera ku Tiyeni
Ku tiyeni Ku Ukwati Tiyeni
Ay Yo! Tiyeni!
Tiyeni! TIyeni! Tiyeni! eish!
Ndiwe mbambande baby
Anthu onsewa akungodabwa tinakumana kuti?
Tinakumana kuti?
Ndiwe mbambande baby
Anthu onsewa akungofunsa kodi tithera kuti?
Kodi tithera kuti?
Ku Tiyeni
Written by: Kelly Kambwiri, Praise Umali, Robert Ching’amba
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...