Lyrics

Tell me what's the problem baby M'mose ndayambila kudikila M'mpaka dzuwa lalowa Ineyo kudikila, mwina ubwela Maso chewu chewu kunjira Maybe utulukila, mwina ubwela Dzulo unati mawa Dzana unati mawa Nanga lero bwanji Tell me what's the problem baby Dzulo unati mawa Dzana unati mawa Nanga lero bwanji Tell me what's the problem baby Kodi ubwela iwe, Kodi ufikadi Ndiyakhule, ndiyakhule Kodi ubwela iwe, koma Ngati wasitha, pulani Ndimasule, undimasule I've been waiting, waiting I've been waiting, waiting, for you Kudikila nkowawa I've been waiting, waiting I've been waiting, waiting, for you Kudikila nkowawa Kapena matola afela panjira Kapena bus break down Nkhawa ya ndigwila Phone yako sikugwila Kapena wakumana ndi dolo wina Wakunyengeze babe mwina wakuwina Wakunamiza sindingakusamale mwina Tell me what's going on oh Dzulo unati mawa Dzana unati mawa Nanga lero bwanji Tell me what's the problem babe Dzulo unati mawa Dzana unati mawa Nanga lero bwanji Tell me what's the problem babe Kodi ubwela iwe, Kodi ufikadi Ndiyakhule, ndiyakhule Kodi ubwela iwe, koma Ngati wasitha, pulani Ndimasule, undimasule I've been waiting, waiting I've been waiting, waiting, for you Kudikila nkowawa I've been waiting, waiting I've been waiting, waiting, for you Kudikila nkowawa
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out