Lyrics

Ouh oh Yeah yeh Yeah I wanna love you in my lifetime I wanna love you in the next one Swear to God I'm done with the silly silly games Ndiwe amene wandisinthisa my ways I've been praying' for a long time I can't believe it now you're all mine I would give it all away in a heartbeat for you Mtima wako undigwilitse Ukamadwala ndiuchilise Tili limodzi usakaike Iwe Kaya nkutali tikafika ife Pali zingapo ndikuziwise Ululu wako ndiuthimise (yeah yeah) Tili limodzi usakaike Iwe Kulikonse tikafika ife One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike Mpaka tika mpaka tika One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike Mpaka tika mpaka tika Nthiti ya nthiti zanga Mnofu waminofu yanga Namalenga anapanga shubu pokulenga Iwe mama Nthiti ya Nthiti zanga Mnofu waminofu yanga Chauta anapanga shubu pokulenga Iwe mama Mtima wako undigwilitse Ukamadwala ndiuchilise Tili limodzi usakaike Iwe Kaya nkutali tikafikaife Pali zingapo ndikuziwise Ululu wako ndiuthimise (yeah yeah) Tili limodzi usakaike Iwe Kulikonse tikafika ife One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike Mpaka tika mpaka tika One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike One, two, three Mpaka tikafike Mpaka tika mpaka tika Mtima wako undigwilitse Ukamadwala ndiuchilise Tili limodzi usakaike Iwe Kaya nkutali tikafikaife Pali zingapo ndikuziwise Ululu wako ndiuthimise (yeah yeah) Tili limodzi usakaike Iwe Kulikonse tikafika ife
Writer(s): Chifuniro Kasiya Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out