album cover
Cup
22
Hip-Hop/Rap
Cup was released on April 20, 2024 by A'ba.lé Sound Systems as a part of the album Chamba 7
album cover
Release DateApril 20, 2024
LabelA'ba.lé Sound Systems
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM93

Music Video

Music Video

Credits

PERFORMING ARTISTS
Mario Bros Mw
Mario Bros Mw
Performer
Krazie G
Krazie G
Vocals
Ace Dirty
Ace Dirty
Vocals
Crispy Malawi
Crispy Malawi
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Chifundo Chingaipe
Chifundo Chingaipe
Songwriter
Francis Costa Vassilatos
Francis Costa Vassilatos
Songwriter
Phineus Moyo
Phineus Moyo
Songwriter

Lyrics

Runner dancehall zau Masicka
Mpasha kupanga kufaka pansika
Unamva za bar yo Pita Muthalika
Ndikomwe ndili pano man kutalika
Ndungo rapper man ndikulalika
Ndilimwamba man mitambo ndabandika
Ati "Spe iwe uzikhalika, osamajama yanga disk yokalika"
Ta winner ndife tipatse cup
Mfana wovaya bwera ndupatse map
Drip on drip ndipatse cup
Fame ukasunge kwanu, ife tipatse guap
Tipatse cup, ndipatse cup
Ndipatse cup
Ta winner ndife, tipatse cup
Mkati kwambiri tatulukamo
Bwanji umadana ndi chulungamo?
Dollar Ya COSOMA kugulira sneaker
Chi beat chokoma kuphulitsa speaker, Mazenene
Ma kicks ndi chidendene
Izi ndizachilengedwe huh
Nabadwa chonchi, game ndi Yao, chaku Mangochi
Ndamgwira thako wagwira ntochi
She gettin' technical ngati ndi Soche
Rap ndatenga ndipatse Trap
Gist ili bho ndipatse sharp
Ma screenshot ayi ndipatse snap
Mfana wothamanga ndipatse lap
Tipatse cup, ndipatse cup
Ndipatse cup
Ta winner ndife, tipatse cup
A Nusaince to the game like Japanese porn
Fuck your opinion, this is rap's very own
Dolo wako ndimupanga chandamale
While I'm smokin' ndine Dube, she fuckin' Bob Marley
Effortless, Leveless
The Devil next city is heat that we droppin'
Don't second guess I like pasta, nde eko verse
This tha Vatican Pope
Ndipatse cup, the drip got it twisted
Ndimpatse tap
Ukandiyesa nde undipatse sup
Kukonda mpasha koma simpatsa Gap
Haa! ndipatse Cup
Written by: Chifundo Chingaipe, Francis Costa Vassilatos, Phineus Moyo
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...