album cover
Lenisa
album cover
Lenisa was released on July 16, 2024 by Bongo Joe as a part of the album Lenisa - Single
July 16, 2024
LabelBongo Joe
BPM192
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Music Video

Music Video

Lyrics

Ndinapeza Nkazi
Ndimange Naye Banja
Ndinapita kwa apongozi
kuka kambirana
Apongozi ndabwera
Chifukwa chamwanayu
Mwana Ndamukonda
Nayeso wandikonda
Apongozi poyankha
Mwanayu tengani
Koma chimodzi chokha inu
Mukasamalire
Ndinapeza nkazi
Ndimange naye banja Lenisa
Koma Lero
Wandichita Lenisa
Lenisa wandithawa
Lenisa wapita
Written by: Yobu Maligwa, Yosefe Kalekeni
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...