Credits

PERFORMING ARTISTS
Willz Mr Nyopole
Willz Mr Nyopole
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Willz Mr Nyopole
Willz Mr Nyopole
Songwriter

Lyrics

Ndimaku, kuku
Ndimaku, kuku
Ndimakumphelerako
Ndimakumphelerako
Ndimakumphelerako
Chauta nkhale wako
Kuti upedze wako
Okonda mutima wako
Ndimakumphelerako
Ngakhale unayenda unandisiya
Ndimakumphelerako
Mulungu yekha ndiye adziwa
Ndimakumphelerako
Tsiku lina ndidzapola
Ndimakumphelerako
Hello hello
Kodi unakwanisa kudzipeza zimene unali kusakila mu chikondi
Ndimangodzimfusa mafunso
Kodi anakupatsa zimene ndinalephera kukupatsa
Kodi nalakwa chani?
Unangondisiya popanda chifukwa ma-ma-ma
Natangwanika, kumbukila mau ako
Ochoka pakamwa pako
Unati sungayende ngakhale mavuto achuluke
Ndimakumphelerako
Chauta nkhale wako
Kuti upedze wako
Okonda mutima wako
Ndimakumphelerako
Ngakhale unayenda unandisiya
Ndimakumphelerako
Mulungu yekha ndiye adziwa
Ndimakumphelerako
Tsiku lina ndidzapola
Ndimakumphelerako
Iye Iye
Kodi umamudza umukonda?
Kodi mtima wako unakondwa?
Kodi ukamulanga mmaso
Umanva chikondi chochoka pansi pamutima
Kodi suzamusiya naye?
Kodi uzaka-kalamba naye?
Kodi nthawi zina mwina umaganizapo
Kuti iwe nane tingabwezani?
Kodi ungakondele nadze
Mwina ingakhale mphatso
Awo ndimaganizo anga
Ndimakumphelerako
Chauta nkhale wako
Kuti upedze wako
Okonda mutima wako
Ndimakumphelerako
Ngakhale unayenda unandisiya
Ndimakumphelerako
Mulungu yekha ndiye adziwa
Ndimakumphelerako
Tsiku lina ndidzapola
Ndimakumphelerako
Ndimakumphelerako
Chauta nkhale wako
Kuti upedze wako
Okonda mutima wako
Ndimakumphelerako
Ngakhale unayenda unandisiya
Ndimakumphelerako
Mulungu yekha ndiye adziwa
Ndimakumphelerako
Tsiku lina ndidzapola
Ndimakumphelerako
Written by: Willz Mr Nyopole, willson ngoma
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...