Music Video

Music Video

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Ino M'bwana
Ino M'bwana
Songwriter

Lyrics

Ino M'bwana
Anasiya kutiyendera
Phone yanga kundiimbira
Ati Level in sitha aah
You Use to be My Friend ehh
Ponda apa ndipondepo ooh
You Use to be My bredman
Bredman
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
For the past 4 years
U where always by my side
Used to talk used to walk
Now you never on my sight
All the memories we had
My boy now its all gone
You got money you got power ****
Oooooh
Now its all done
You dont call my phone
Cause you way up
Oooooh
Now its all done
I got left with the memories
Oooooh
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
Ndikaimba phone imangoti busy
Mwina munandiika blacklist mundiuze
Mwina zinaku bowani zimene ndinapanga
Mwaiwala kale munagwilira cross yanga
Pano munachuka mukuone pa twitter pa TV
Galimoto muyendera ndi massive
Abale mwatithawa afriend mwatitaya
Why for this? why for that?
Mwaiwala munatenga ndalama zanga
Why for this so? Why for that?
Mwaiwala munagwira sister wane
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
Owowo
Owowo
Anangosala Ndi ma Memories
Memories
Ntima kuwawa ndi ma Mamories
Mamories
Anangosala Ndi ma Memories
Ino M'bwana
Written by: Ino M'bwana
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...