album cover
Nena
1
Afro-Beat
Nena was released on December 5, 2024 by Lizgo Agency as a part of the album Lost Spaceman
album cover
Release DateDecember 5, 2024
LabelLizgo Agency
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM101

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Otis Dean Massoudih
Otis Dean Massoudih
Songwriter

Lyrics

Yandipeza nkhani
Akuti ukumandiyenda m'mbali
Is it why ukungomakhala busy
These days sukumandipatsa nthawi yako
Unkayimba ma foni, ma foni
Umati where are you
Baby come and see me
Now I'm lonely, lonely
Ndikamakufuna sukumapezeka
Ngati ukukondanaso ndi munthu wina
Let me know, ndidziwe
Maybe chikondi changa chasiya kukoma
Let me go, ndiyende
Tisamangotaitsana nthawi ndiwuze
No don't you lie, funa ndidziwe
Mwina vuto ndi ine nena nena nena
Ngati ukufuna ndichoke nena nena nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena
Mwina vuto ndi iwe nena nena nena
Kodi umandifunabe nena nena nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena nena
Ndakananga ndi ma frenzo
Ambilimbili pamene ndima defender iweyo
Molo mopanga za ineyo
Ndinali busy kufinyika kupanga za iweyo
Zoti ndimakukonda anthu amadziwa
Daily ndimakuwonetsa
Koma kwa azinzako akamafunsa ukumandibisa
Ngati paliso wina
Let me know, ndidziwe
Maybe chikondi changa chasiya kukoma
Let me go, ndiyende
Tisamangotaitsana nthawi ndiwuze
No don't you lie (No) funa ndidziwe
Mwina vuto ndi ine nena nena nena
Ngati ukufuna ndichoke nena nena nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena
Mwina vuto ndi iwe nena nena nena
Kodi umandifunabe nena nena nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena nena
Nena nena (Nena) Nena (Nena) Nena nena
Written by: Otis Dean Massoudih
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...