Credits

PERFORMING ARTISTS
Paul Payne837
Paul Payne837
Lead Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Penyani Phiri
Penyani Phiri
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Paul Payne837
Paul Payne837
Recording Engineer
Penyani Phiri
Penyani Phiri
Graphic Design

Lyrics

Muntu wanga uli munyimbo
Ndikukumbukira iwe lero
Mutima usakila chikondi
Chikondi chako ndichisomo
Masiku upaka nakuyewa
Ndimafuna che kukuona
Umandipangitsa kumvela bwino
Ndilota ndi cheza nawe patelefono
Ndakusowa iwe chikondi
Mutima wanga uli mu motto
Usiku onse ndikuyewa
Kumwamba kwasoba nyenyezi
Ndakusowa iwe chikondi
Mutima wanga uli mu motto
You stuck on my mind babe I miss you bad
My world stood still you my helipad
My ride or die am flying solo
Hate my favorite meal with no coleslaw
Like the lambo with no gasoline
Babe tell me what's the point of me looking clean?
Who's the lion King? With a missing Queen
Simba misses you Nala where you been?
Ndakusowa iwe chikondi
Mutima wanga uli mu motto
Usiku onse ndikuyewa
Kumwamba kwasoba nyenyezi
Ndakusowa iwe chikondi
Mutima wanga uli mu motto
Muntu wanga uli munyimbo
Ndikukumbukira iwe lero
Mutima usakila chikondi
Chikondi chako ndichisomo
Masiku upaka nakuyewa
Ndimafuna che kukuona
Umandipangitsa kumvela bwino
Ndilota ndi cheza nawe patelefono
Muntu wanga uli munyimbo
Iwe lero
Mutima usakila chikondi
Chako ndichisomo
Masiku upaka nakuyewa
Written by: Penyani Phiri
instagramSharePathic_arrow_out

Loading...