album cover
Limba
album cover
Limba was released on February 3, 2025 by 2043704 Records DK as a part of the album Limba - Single
February 3, 2025
Label2043704 Records DK
LanguageEnglish
BPM
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Music Video

Music Video

Lyrics

Ritaa
Sispence
Ndabalalika kukhulupira abale
Ndamalizika kukhulupira chikondi
Zonse zinathera kufuna kundichotsera Moyo
Zonse zinathera kufuna kundichotsera Moyo
Ukhala wekha? Udzakhala apapa
Uvina wekha? Udzaima apa hmmm
Tiyemo! Nditsala ndipume
Yes or no? Ukudziwa kale
Maso anatopa kulira
Mtima nkufika polimba
Sungaswe chinthu choti nchosweka kale
Pano mtima unalimba
Maso anatopa kulira
Mtima nkufika polimba
Sungaswe chinthu choti nchosweka kale
Pano mtima unalimba
Akaona ndili ndekha daily
Ena amangoti ndine odzikonda ineyo
Betrayal yonse inabwera my way
Ondipereka ineyo anali anzanga omwewo
Nde zachikondi, ndikazimva
Ndikazimva sindifunanso
Ukhala wekha? Udzakhala apapa
Uvina wekha? Udzaima apa hmmm
Tiyemo! Nditsala ndipume
Yes or no? Ukudziwa kale
Maso anatopa kulira
Mtima nkufika polimba
Sungaswe chinthu choti nchosweka kale
Pano mtima unalimba
Maso anatopa kulira
Mtima nkufika polimba
Sungaswe chinthu choti nchosweka kale
Pano mtima unalimba
I'm living my life
Enjoying my life
I'm living my life
Enjoying my life
Zonse zonse, ndinazitaya
Zonse zonse ndinaziiwala
zonse, ndinazitaya
Zonse zonse ndinaziiwala
Maso anatopa kulira
Mtima nkufika polimba
Sungaswe chinthu choti nchosweka kale
Pano mtima unalimba
Maso anatopa kulira
Mtima nkufika polimba
Sungaswe chinthu choti nchosweka kale
Pano mtima unalimba
Written by: Rita Mwantalli
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...