album cover
Lero
185
Afro-Beat
Lero was released on March 17, 2025 by 8787965 Records DK as a part of the album Lero - Single
album cover
Release DateMarch 17, 2025
Label8787965 Records DK
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM89

Music Video

Music Video

Credits

PERFORMING ARTISTS
innocent Nyanda
innocent Nyanda
Background Vocals
COMPOSITION & LYRICS
innocent Nyanda
innocent Nyanda
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
innocent Nyanda
innocent Nyanda
Producer

Lyrics

One heart one vision
Nyandah
Unali owina padzana
Unkawonetsa chikondi padzana
Kuyenda limodzi padzana
Kenaka kundisiya
Ndinalimba mtima
Kukhala ndekha
Moyo unkavuta inde
Koma ndinakhalabe
Papita zaka lololo
Ukubwera ndi nkhongono
Wati ukufuna mtima wanga
Ine no no no
Papita zaka lololo
Ukubwera ndi nkhongono
Wati ukufuna mtima wanga
Ine no no no no no no
Usandikonde leeee lero ine
Pazonse unachitaaaaaa
Mtima nakufufuta ine
Usandikonde leeee lero ine
Pazonse unachitaaaaaa
Mtima nakufufuta ine
Eya ma memories onse
Anachoka now I don't care
Unapanga zambiri zondinyasa
Ubwino wako onse unachoka
Zoti ungakondeso ndimakayika
Unavulaza mtima wanga
Kuwusiya ndi bala
Ndinayesa uchondelera
Koma unazitenga zambwelera
Mpakana ndinabwelera
Sunandipase mpata
Papita zaka lololo
Ukubwera ndi nkhongono
Wati ukufuna mtima wanga
Ine no no no
Papita zaka lololo
Ukubwera ndi nkhongono
Wati ukufuna mtima wanga
Ine no no no no no no
Usandikonde leeee lero ine
Pazonse unachitaaaaaa
Mtima nakufufuta ine
Usandikonde leeee lero ine
Pazonse unachitaaaaaa
Mtima nakufufuta ine
leeee lero ine
Pazonse unachitaaaaaa
Mtima nakufufuta ine
Usandikonde leeee lero ine
Pazonse unachitaaaaaa
Mtima nakufufuta ine ine
Written by: innocent Nyanda
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...