album cover
Che N'dogo
44
Afro-Beat
Che N'dogo was released on June 2, 2025 by Ell Macuinjinho as a part of the album Che N'dogo - Single
album cover
Release DateJune 2, 2025
LabelEll Macuinjinho
LanguagePortuguese
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM93

Credits

PERFORMING ARTISTS
Ell Macuinjinho
Ell Macuinjinho
Performer
Big Dan
Big Dan
Electric Fretless Guitar
COMPOSITION & LYRICS
Razaque Macuinja
Razaque Macuinja
Songwriter
Daniel Chithime
Daniel Chithime
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Big Dan
Big Dan
Producer
Azique Ndala
Azique Ndala
Co-Producer

Lyrics

BASE 1
anali nzanga uyu
pamene ndimaponda wapondepo,
amandivinikila, pamene thupi langa lava mphepo
ndiyemwe amandiptsa ntadji
munthumba mwanga mukayaba kushota
ndiyemwe amathilira madzi
kaduwa kanga kakayamba kufota
anali central defender
pa mavuto komanso matenda
kundilimbitsa nditsatope
kundiimitsa ndikaponda matope
komaaa
chipongwe emwe akupanga ndi okondedwa
amakuoanga chipongwe ndikuthawa ndi okondedwa
no, nooo
okondedwa
CORO 1
che n'dogo
che n'dogo
che n'dogo
mwandiswera ntima maikoto
che n'dogo
che n'dogo
che n'dogo
kusewera sasewera chontcho
BASE 2
sindikanalira chontchi
ukanakhala siwe nzanga wapantima
sindikanatulutsa nsonzi
zikanakhala zochita munthu wina
m'mano mwanzako
sungamatosemo mitengo
m'maso mwanzako
sungamatosemo mitengo
wamenya yobela
kutsewera samafinyana kumphuno
akadzi onsewa
waona chani kwa lamwako?
amuna onsewa
nyumba yanga wasandutsa nyumba yako
Written by: Daniel Chithime, Razaque Macuinja
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...