Music Video
Music Video
Credits
PERFORMING ARTISTS
Teddy Makadi
Vocals
ViddiX
Vocals
COMPOSITION & LYRICS
David Phiri
Songwriter
Teddy Maliza
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Benji.
Producer
Melma
Engineer
Lyrics
Ooh woah yeah
I don't need too much from you
Chabe ndimafuna your attention
Baby we like sticks and glue
Pomwe tizawolele ndipowepo and
Every time I think of you
Mutu sumagwila uwu
And every time I think about you
Uziutenga mtimawu
My friend forever
Ndiwe wanga
Ndizikamba mobwenza
Mpaka mpaka
Cause every time I think of you
Mutu sumagwila uwu
And every time I think about you
Uziutenga mtimawu
Kulibe kwina I would rather be
Kuposa muchikondi nawe baby
Ine ndi CEO iwe ndi company
Ndufuna kuhamba nawe
Kuchoka pansi pa mtima
My love sindizamupatsa wina
Ndipo azadalitsa pa guwa
My friend forever
Ndiwe wanga
Ndizikamba mobwenza
Mpaka mpaka
Cause every time I think of you
Mutu sumagwila uwu
And every time I think about you
Uziutenga mtimawu
Cause every time I think of you
Mutu sumagwila uwu
And every time I think about you
Uziutenga mtimawu
Uziutenga
Uziutenga
Uziutenga
Uziutenga mtimawu
Written by: David Phiri, Teddy Maliza