album cover
Pang'ono
album cover
00:00
00:05
00:30
00:50
00:55
01:10
01:15
01:20
01:35
01:50
01:55
02:40
02:55
03:10
03:30
00:00
03:36
Past 7 Days
Pang'ono was discovered most frequently at around 55 seconds into the song during the past week

Lyrics

Ikon wafika, no ID chinzika
Ikon wafika (Ayo Billy), Ikonini
Ayi!
Dzulo ndimati mowa ndaleka, mowa ndaleka (Ayi!)
Leroli ndingofuna macheza
Ndimati mowa ndaleka, mowa ndaleka
Leroli ndangobwelera shisha
Ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
Koma mowa si madzi

Ndikati DJ tangokweza pang'ono, ndingovina pang'ono
Sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
Ndungofuna pang'ono (Oh)

Ndungofuna pang'ono
Ndikati DJ tangokweza pang'ono (Kwambiri Ayi), ndingovina pang'ono (Pang'ono)

Ndungofuna pang'ono (Kwambiri Ayi)
Sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri (Pang'ono basi), ay
Ndungofuna pang'ono
Ndungofuna pang'ono, pang'ono, pang'ono, pang'ono
Ndungofuna pang'ono, pang'ono, pang'ono, pang'ono, pang'ono
Ndungofuna pang'ono basi
Ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
Koma mowa si madzi
Ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
Hoza, hoza iwe! iwe! hoza, hoza
Hoza, hoza iwe! iwe! hoza, hoza awuze
Hoza, hoza, hoza, hoza
Hoza, hoza, hoza,hoza awuze
Ndazindikira kwacha
Phone yasowa, ndalama ndilibe
Ndiyenda bwanji apa? (Mayi ine, mayi ine)
Ndazindikira kwacha
Phone yasowa, ndalama ndilibe
Ndiyenda bwanji apa? (Mayi ine, mayi ine)
Ndikati DJ tangokweza pang'ono, ndingovina pang'ono
Sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
Ndungofuna pang'ono (Oh)
Sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
Ndungofuna pang'ono
Ndikati DJ tangokweza pang'ono (Kwambiri Ayi), ndingovina pang'ono (Pang'ono)
Sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri, ay
Ndungofuna pang'ono (Kwambiri Ayi)
Sindimasuka kwambiri ndingomwako uwiri (Pang'ono basi), ay
Ndungofuna pang'ono
Ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
Koma mowa si madzi
Ndazazindikira kuti pondichera ndinamwa mwamacheza
Koma mowa si madzi
Written by: Joseph Chilabade
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...