album cover
A Joany
album cover
A Joany was released on November 14, 2025 by Kuwala Entertainment as a part of the album The Best Vol. 1
November 14, 2025
LabelKuwala Entertainment
LanguageEnglish
BPM119
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

A Joany
Ngatitu mukufuna
Kuti moyo wanu moyo wamtsogolo udzakhale wabwino
A Jackie
Ngatitu mukufuna
Kuti moyo wanu moyo wamtsogolo udzakhale wabwino
Muyenera kutsata ooh oh
Moyo wachikhristu womwe tingapemphe kwa Mulungu Atate
Muyenera kutsata ooh mama eh
Moyo wachikhristu womwe tingapemphe kwa Mulungu Atate
Takondwa mzanga eh
Takondwa kumva kuti
Iih amama eh mwayambadi kutsata
Ooh amzanga eh owooh Yesu Khristu
Ndi njira iyo ndi njira ya kumwamba
Kuwala mzanga kuwala kwa padziko
Chitsime icho chitsime cho cha moyo
Takondwa mzanga eh
Takondwa kumva kuti
Iih amamah mwayambadi kutsata
Ooh amzanga eh owooh Yesu Khristu
Ndi njira ndi njira ya kumwamba
Kuwala mzanga kuwala kwa padziko
Chitsime icho chitsime cho cha moyo
Takondwa mzanga eh
Takondwa kumva kuti
Iih amamah mwayambadi kutsata
Ooh amzanga eh owooh Yesu nKhristu
Ndi njira iyo ndi njira ya kumwamba
Kuwala mzanga kuwala kwa padziko
Written by: Paul Banda
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...