album cover
YOUR TiME
2
R&B/Soul
YOUR TiME was released on January 21, 2026 by BVRELYSOBVGVNG WORLDWIDE/TURNUP MUSIC as a part of the album Another Playlist Just For Her - EP
album cover
Release DateJanuary 21, 2026
LabelBVRELYSOBVGVNG WORLDWIDE/TURNUP MUSIC
LanguageEnglish
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy
BPM89

Credits

PERFORMING ARTISTS
DBturnUp
DBturnUp
Rap
COMPOSITION & LYRICS
Dearborn Chris Malindah
Dearborn Chris Malindah
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
BlackT
BlackT
Engineer

Lyrics

(Indistinct phone conversation)
Choyamba ndithokoze arigato
Nkazi oti ndikufila naye sitomato
Mwana oyaka Moto sindukamba za tobacco
You make that fruity shake tidyeleko ma somango
Siiwe Cris or czar Komabe ukali wako
Wavala zi new drip uoneka za kariakooo
Umaona kuti wayesesa kumbali yako
let you lead the way utanyamula nyali yako
Chomwe ufuna ndinthawi yako
Ungofuna ntakupasako nthawi yako
Chomwe ukufuna iweyo ndi nthawi yako
Ungofuna nditamakupasa nthawi yako
Amvekele umandigwesa timphwayi tako
Umakonda kuti uzingopanga zako zako
Ine Ndikuziwa kuti iyi ndinthawi yako
Ndingofuna utandipasako nthawi yako
Tandihalako
Ndili ndekha cha pa crib tandigwilako
Umakonda zobwela mochedwa lawilako
Ndikuziwa ukuvepa koma tangothawilako
Amene sakufila ndiye alipo angapo
Ndimaziwa ndine opp mmaso mwa anzako
Sooner or later ndikafika kwa mayi ako
Ain't no need to worry ineyo ndi guy wako
Bwenzi lopanda sankho
Pankhani ya iwe ndimakhala nchosatha chilako
Masewela ake ogwilana gwilana ndi chipako
Ka portable bho kwa ineyo ndi chi thako
Lero Nde Wabwela wekha izozo Nde ndizako
Tikhalila kuphana iwe Ine sinzako
Umandifiuna ineyo koma tipanga zako
Zomwe nditakupange ukandineneza kwa amako
She getting impatient
We Fell for temptation
Indulge in relations
Better Check duration
Can't fold under pressure
I ain't tryna stress nah
Had to learn my lesson
Had to learn your ways
Chomwe ufuna ndinthawi yako
Ungofuna ntakupasako nthawi yako
Chomwe ukufuna iweyo ndi nthawi yako
Ungofuna nditamakupasa nthawi yako
Amvekele umandigwesa timphwayi tako
Umakonda kuti uzingopanga zako zako
Ine Ndikuziwa kuti iyi ndinthawi yako
Ndingofuna utandipasako nthawi yako
Nthawi yako
Nthawi yako
Nthawi yako
Nthawi yako
Ndipase nthawi yako
Nthawi yako
Ndipase nthawi yako
Ndufuna nthawi yako
Written by: Dearborn Chris Malindah
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...