album cover
Vision
album cover
Vision was released on January 10, 2025 by Bless Williamusic as a part of the album Back to back EP
January 10, 2025
LabelBless Williamusic
LanguageEnglish
BPM97
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Yeah yeah yeah
Na-na-na na-na-naah
Bless
Mmhh
Yathu ija ma mission
Pena timangogwera, pena kumayendera vision
Ambiri amabwera ngati atikonda kenako atiyuze
Amadziwa geli tinavaya, koma tilibe kanthu
Nde basi atizunze
Koma tidzayiphula ndi one day
Sitikutopa
Mpaka lusoli litikankhe
Ichichi ndichidziwa
Mulungu sataya wake
Lembo limanena
Siliva ndi golide ndi zake
Yeah yeah
Kunena mosanama
Luso tilinalo, ndipo tili ndi khama
Koma hmm
Yavuta ndi ndalama
Nanji enafe paja tili ndi mafana
Nde
Ndimangogogoda chitseko
Kuti mwina zinthu zisintheko
Koma namondwe ndi mphepo
Zapangitsa moyo usintheko
Ndeno mukandiwona ku nseu
Mukumati ndilibe nzeru
Munthune ndili ndi mbeu
And I've got the capacity
Koma tidzayiphula ndi one day
Sitikutopa
Mpaka lusoli litikankhe
Ichichi ndichidziwa
Mulungu sataya wake
Lembo limanena
Siliva ndi golide ndi zake
Yeah yeah
Ndimangogogoda chitseko
Yathu ija ma mission
Kuti mwina zinthu zisintheko
Pena kumayendera vision
Koma namondwe ndi mphepo
Nkumadzimvera chisoni
Zapangitsa moyo usintheko
Koma tiri ndi VISION
Ndi one day
Litikankhe
Mulungu sataya wake
Siliva ndi golide ndi zake
Written by: Blessings William Namaombe
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...