album cover
Mbuzi
album cover
Mbuzi was released on May 23, 2023 by Wazizur as a part of the album Tailora
AlbumTailora
May 23, 2023
LabelWazizur
BPM74
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

I'm the goat that's why God leads me to greener pastures
Graduating soon and soon I'll be owning my masters
I'be smiling always got it from my mama uhh
Blessings homie tikuphaka pizza wa pa
Argh
Broken hearts are mended ndiwa zatheka bwanji
He's Jehovah Jireh can't frustrate his plans
He can use my pain to write my story sweetest one
I am the proof of his existence n'navomera kalelaleeee
Kungopunthwa dziko limangoti sharp ada
Iwe zako ada zathapo utha kugwira njakata
Amakutcha goat uli pa top ada
Ukangotha umangomva awanso mxi
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Iwe mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Iwe mbuzi yopanda Kanthu
Mbuzi yopanda
I went silent for a bit
Now it's fire in the booth I am dropping gems I hate diseases
Palibe azakumbuke unali dolo in 50 years
Nothing new under the sun osamapakana ma pears
Kungopunthwa dziko limangoti sharp ada
Iwe zako Ada zathapo utha kugwira njakata
Amakutcha goat uli pa top ada
Ukangotha umangomva awanso mxi
Mbuzi Yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Iwe mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Mbuzi yopanda kanthu
Woah
Iwe mbuzi yopanda kanthu
Mbuzi yopanda
Written by: Aubrey Suffix Ghambi

Loading...