album cover
Mphungu
album cover
Mphungu was released on June 12, 2026 by It's Only Entertainment as a part of the album Mphungu
AlbumMphungu
June 12, 2026
LabelIt's Only Entertainment
LanguageEnglish
BPM92
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

(Mphungu screeching)
Meeeeeeeh eeeh
Hehehe hahahahahahahaha
Yeah
(Mphungu screeching)
Yeah
Very Good Very Good
Ndili pa Mugg & Bean kumwa cappuccino
Kulingalira momwe ndi run'ire chaka chino
Kupanda ndalama ndi ululu wa dzino
Nane ndimafuna zi ma Versace ndi Moschino
Ndipange bwanji pamenepa ndilowere kuti
Ndamva kuti ndalama zili mu nthaka ndikalime?
Ndipange bwanji ndikhalebe wa mu office wa suit
Ndipange za chakudya cha pansi olo pa lilime?
Hustle tikupanga palibepo zogona
Pakati pa ziminga ndi njuchi pali zonona
Ndikhale home owner komanso a business owner
Kutukula nawo dziko osamangodikila SONA
Koyambira zonse ndi ku Mphungu
Mphungu Mphungu Mphungu Mphungu
Zaka zapita pano ndine Mphungu
Mphungu Mphungu Mphungu Mphungu
Kuyionera patali game
Timasewera pamwamba ngati Mphungu (Mphungu)
Tachoka nazo kutali
Zimafunika ma discipline ngati Mphungu (Mphungu)
Yeah
Yeah
Okay
Ndili pa khonde ndati ndidyeko ka ganja
Kulingalira kodi chaka chinochi ndisanja
Palibe amene struggle yake imamuyanja
Tonse timakufuna ku Dubai ndi ku nyanja
Kuimba ndinayamba pa desk ndi Themba
Pa break tikudya mandasi freezes ali 10 ba
Ndimakumbukila break ya 20 minutes
Imakhala after mathematics nthawi 10 bar
Yemwe ali Mphungu ndekuti ndi visionary
Azapanga zinthu zazikulu before the obituary
Mapemphero kwa Mulungu very necessary
Kuli ma sukulu ambiri Mphungu ndi Legendary
Koyambira zonse ndi ku Mphungu
Mphungu Mphungu Mphungu Mphungu
Zaka zapita pano ndine Mphungu
Mphungu Mphungu Mphungu Mphungu
Kuyionera patali game timasewera pamwamba ngati Mphungu (Mphungu)
Tachoka nazo kutali zimafunika ma discipline ngati Mphungu (Mphungu)
Written by: Noel Phyzix Chikoleka
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...