album cover

Mulimi

91Afro-Pop2026
album cover
Mulimi was released on May 20, 2026 by SLEYAN ESSENTIALS as a part of the album LOI
AlbumLOI
ReleasedMay 20, 2026
LabelSLEYAN ESSENTIALS
LanguageEnglish
BPM81
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Mmmm
Mulimi akadzala mbeu sayifukula
Ayithilila nayang'anila
Sakumba kuti aone meneyikulila
Amathila manyowa, nalindila mvula
Ndipo mbeu yikamela
Mulimi asangalala
Podziwa thukuta lake
Silinapite pa chabe
Ndipo akakolola, adya ndi banja lake
Zikachuluka, zina agulitsa
Khalani patience ngati mulimi
Dzala ngati mulimi
Thilila ngati mulimi
Palila ngati mulimi, yeah
Dikila ngati mulimi
Ndupemphera ngati mulimi
Ndipo uzakolola
Ukalimbikila, suzasowa kanthu
Ndipo mbili yako yizamveka
Kuma area, kumbukila mau anena
Uzadya thukuta lako
Yehova azadalitsa, ntchito za manja ako
Ndipo mbeu yikazamela
Uzasangalala
Kuti thukuta lako, silinapite pa chabe
Khalani patience ngati mulimi
Dzala ngati mulimi
Thilila ngati mulimi
Palila ngati mulimi, yeah
Dikila ngati mulimi
Ndupemphera ngati mulimi
Ndipo uzakolola
Khalani patience ngati mulimi
Dzala ngati mulimi
Thilila ngati mulimi
Palila ngati mulimi, yeah
Dikila ngati mulimi
Ndupemphera ngati mulimi
Ndipo uzakolola
Ndipo mbeu yikamela
Mulimi asangalala
Podziwa thukuta lake
Silinapite pa chabe
Ndipo akakolola, adya ndi banja lake
Zikachuluka, zina agulitsa
Khalani patience ngati mulimi (uh)
Dzala ngati mulimi (uh)
Thilila ngati mulimi (uh)
Palila ngati mulimi, yeah (yeah)
Dikila ngati mulimi (ndipo uzakolola)
Ndikupemphela ngati mulimi (ndifya ndi banja langa)
Ndipo uzakolola (zikachuluka, zina ndikulitsa)
Written by: loiswayo alvin roben

Shazam Footer

Select language:
Google Play Store
Apple App Store
Chrome Web Store
Galaxy Store

Follow Us

Loading...