album cover
Muzandifuse
album cover
Muzandifuse was released on October 30, 2025 by PaKaya as a part of the album Muzandifuse - Single
October 30, 2025
LabelPaKaya
LanguageEnglish
BPM89
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Chilako lako chachikodi chatha
Ndikakumbukila zomwe unandipanga
Ndikakhala ndimagwidwa ndimantha
Sindifuna wina kumpasa danga
Wandifoola--wandibela mtendele
Bola ukananena-pano nditapeza wina
Pre-hook
Wanditaitsa nthawi _yanga
Wandionetsa khiyama
Zina umangoona waziyamba
Wandisiya mmalele
Mkazandiona
Ndikupanga zachikondi mzandifutse
Mkazandiona
Ndikupanga zachikondi mzandikumbutse
Poti zonse zimachitika chimodzi modzi
Zomwe timachitazose nazichita kale
Zimachitika zose chimoz moz
Njila timadutsa ine naidutsa kale
Chonde mtima wanga dekha
Sikoyamba kuona mkazi okongola
Chonde mtima wanga dekha
Sikoyamba uona mkazi wachiko-ka
Ndatopa kumangolila lira
Kukhalira kudandaula
Ndatopa kumango khumudwa
Single life ndizitolera
Wanditaisa nthawi yanga
Wandionesa khiyama
Dzina umangoona waziyamba
Wandisiya mmalele
Written by: Kennan Longwe, Sothini Mbizi
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...