album cover
Member
album cover
Member was released on May 24, 2026 by Nino Scottie Exclusively Distributed By TrapRelatedActivities. & ForbesCulture as a part of the album 12th May - EP
May 24, 2026
LabelNino Scottie Exclusively Distributed By TrapRelatedActivities. & ForbesCulture
BPM74
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Music Video

Music Video

Lyrics

We got Curster on Keyz
Ay Forty why don't you kill these **** by making another one?
Life is good, Jah Jah wawunika
Trap yako ndiyo wewa, mwina sumadziwa
Ukungofunika uwone kuti tinapita, at the top Koma si Arsenal
What's the plan? lero ndi betcheso, I need the rack
To keep stayin' ahead hundred K a feature
Sindibwata ulere ngati ufuna obowoleze, tangonena ndibwere
Kamafuna ndizikanedza koma kamandizemba
Kamayesa kuti ndingonedza
That's right baby girl ndingonedza
I ain't tryna fall in love si ine member
That's right baby girl ndingonedza
I ain't tryna fall in love si ine member
Huh si ine member, member
Si ine member
Yeah si ine member, member
Yeah, si ine member
I ain't tryna fall in love si ine member
I remember,ndinkabwera pamaso pako ndiyodekha
Umandipepusa, umayenda chozemba
Huh, i appreciate, yeah
Amatenga pang'ono ndawatengera patali
Ndayikokelera pano, zochita kupanga
Kuthamangisa bale, ndilibe nthawi yongokhala
Kundihalla wrong number nthawi ina sindikuyankha
Ma busy okhaokha maganizo pa kwacha
Ndipotose akaka zizikhala mu gaza
Ma busy okhaokha ngati zandiphwanya
Kufila za mkati, sindingashale njapa
Kuwamvetsa kukoma olo adani anga, umpeze, si ine member
Chomwe ndimafuna pa iwe ndikunedza
I'm tryna fall in love, si ine member
Chomwe ndimafuna pa iwe ndikunedza
That's right baby girl ndingonedza
I ain't tryna fall in love si ine member
Huh si ine member, member
Si ine member
Yeah si ine member, member
Yeah, si ine member
I ain't tryna fall in love si ine member
Written by: Allie Nino Junior Ndaila Forbes Onani

Loading...