album cover
Ichichi Interlude
album cover
Ichichi Interlude was released on September 15, 2026 by Baxxy Mw 2026 Noble Music Distro as a part of the album Some Things Take Time
September 15, 2026
LabelBaxxy Mw 2026 Noble Music Distro
LanguageEnglish
BPM108
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

Ukakwera njale uzimwera ichichi
Kuyenda wapansi uzimvera ichichi
Kaya mukuchilla muzimvera ichichi
Ukakhala pa easy nyimbo yake ndi iyiyi
Ukagwira aux uzifaka ichichi
Kaya pa Bluetooth anthu amvere ichichi
Ngati uli DJ yambitsa ndi ichichi
Faka sound kuchoka LLz mpaka ku Mchinji
Ngati Simon Petro undipatse khutu
Utha kuyimba nawo olo kugwedeza mutu
Osawerenga anzako, uwerenge ma buku
Uzipanga zako, focus on what you do
Uzimvera nyimbo osamvera mabodza
Uzingoyikoka, usamakonde kukoka
Zina kumazipewa anthu akamukododga
When the grass gets green kumabwera zinjoka
Uziwerenga mawu osati anzako iwe
Ndakuuza kale kukonda matako iwe
Uyu wagwira, winanso chipako iwe
Moyo ndikamodzi udzapita nako iwe
Jah patsogolo osayiwala kupraisa
Osamakwiya nsanga mtima kumaupeza
Cut to the chase ukhale mfana oleza
Uzilimbikira adzakudziwe ku Dzenza
Sunga pakamwa anthu alibe chisinsi
Usaononge dzina aise mbiri nkachiphwisi
Anali anzako lero avunga ma dissi
Tryna test you kukupanga madissi
Ukakwera njale uzimwera ichichi
Kuyenda wapansi uzimvera ichichi
Kaya mukuchilla muzimvera ichichi
Ukakhala pa easy nyimbo yake ndi iyiyi
Ukagwira aux uzifaka ichichi
Kaya pa Bluetooth anthu amvere ichichi
Ngati uli DJ yambitsa ndi ichichi
Faka sound kuchoka LLz mpaka ku Mchinji
Written by: Happy Titani Bakolo, Lester Ley C Chithando, Stuart Ngundende Jr
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...