album cover
Vip
album cover
00:00
00:05
00:25
00:45
01:10
01:30
01:55
02:00
02:15
02:20
02:40
02:45
03:05
00:00
03:25
Past 7 Days
Vip was discovered most frequently at around 45 seconds into the song during the past week

Music Video

Music Video

Lyrics

Ok tiyambe
Okay, okay
One time, one time
Somebody say hallelujah
There's enough spiritual and moral power in this stadium tonight
That could change the nation
And change the world for jesus Christ
Young people all over the world are marching for every cause in the world
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Kuno kwapenga ndimwana wa a pastor
Akungo itanisa zima shots
Kuno wakomesa ndimwana wa a pastor
Sindika snitcher, uyu ndi homie
Sindimadziwa amatha kuvina
Amapiano atakwera pa sofa
Phone yake wangoikweza ndege
Big man yake kuno singamupeze
Ali ku VIP, ku VIP
Aku blacker ndima minister
Ku VIP, ku VIP
Kuno zithunzi sindika posta
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Aliku VIPzzo
Aku trapper ndi Lizzo ndi Njuchizzo
Vibe ndi nyanja, mazaza ndi zi vinyo
Aliyense ali ndi gibar tili bino bino
Mwana wa abusizzo sakuthawa mowa akuyika ma tisho
Ku party aliyense amakhala single
Crisha and Bebeski ali pa chi mission
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Whattie doskie, ziyana zapenga tiku trappisa Njuskie
Sindiyenda holy ganjah ili mujuzi
$ino gatti sauce, makape alibe olo nsuzi
Kuno ndima bozonke tikuphana duziduzi
Ndilinker nonse iwe ndi bestie
Mwana wa abusa wapenga ndima verse
Uyu ndi nyombe akukomola usipe weziwezi
Kuno siku church utrappe ndima gents
Session yama slizzo udye nyakazi
Makape utsike ukwere ife ngat kabanza
Ma Snow bizzo, mbuyo zikunjanja
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Mwana wa abusa ali ku VIP
Umuzape ku VIP
Alikuma sofa ndima bestie
Wangoti kuno siku church
Written by: Chifuniro Magalasi, Emmanuel Jameson, Huzfy Alie
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...