album cover
Fatima
album cover
Fatima was released on October 15, 2026 by Difusic as a part of the album Fatima - Single
October 15, 2026
LabelDifusic
BPM154
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Lyrics

verse 1:
fatima
ati mmamuwaza samafila bwino mumtima
azapanga zaineyo ndithu tsiku lina
namuuza nakwatila namuuza eee
namuuza nakwatil
komabee
anatumiza text akuti tikumane
kutseli kwa church ine ndati ndipite
akazanga mbwee, ine mbolaye
ndati apa tita apa tita
hook:
wandithesela banja fatima (nadya mchuno mwako)
wandithesela banja fatima (nadyambo mwemoooo)
wandithesela banja fatima (nadya mchuno mwako)
wandithesela banja fatima (apa titaaaa)
mesa wandithetsela banja ndiweyo (ndyeno apa titaaaa)
mesa wandithetsela banja ndiweyo ( apa titaaaa)
ndyeno undiuuze x2
poti wandithetsela manja ndiweyo
verse 2:
ngwengwerengwe ngwengwe ngwengwe
ngwengwerengwe ngwengwe ngwengwe
paja unamatsweda bwera kuzandithetsela banja
lero unditenge iwe
ngat ufuna mtendere
pam'gong'o samtengere
tipange chimvano cha nyerere
ngwengwerengwe ngwengwe ngwengwe
ngwengwerengwe ngwengwe ngwengwe
ngwengwe ngwengwe ngwengwe ngwerengwe ngwengwe
fatima fatima
sukuyankhula zomveka fatima
hook:
wandithesela banja fatima (nadya mchuno mwako)
wandithesela banja fatima (nadyambo mwemoooo)
wandithesela banja fatima (nadya mchuno mwako)
wandithesela banja fatima (apa titaaaa)
mesa wandithetsela banja ndiweyo (ndyeno apa titaaaa)
mesa wandithetsela banja ndiweyo ( apa titaaaa)
ndyeno undiuuze x2
poti wandithetsela manja ndiweyo
Written by: Thokozani Nkuziwaduka

Loading...