album cover
Vama Hate
album cover
Vama Hate was released on October 16, 2026 by Crispy Malawi as a part of the album MAGOGO
AlbumMAGOGO
October 16, 2026
LabelCrispy Malawi
BPM64
Melodicness
Acousticness
Valence
Danceability
Energy

Music Video

Music Video

Lyrics

I'm a hustler baby
Ayo Landie
Dekha ndingo hasser baby
Kuthamanga, thamanga n'town kukana kungokhala
Mmutu mwanga mumangoyenda hustle
Mwana kuthana naye pompo pompo azivaya
Ndilibe nthawi yama cuddles
Vama Love sindikupanga nawo
Bola dollar zanga kumazipanga double
Vama Hate sindikupanga nawo
Nde ndufuna ukauzane ndi anzako
Vama aah nawo
Baby girl ndungofuna kudyako, huh
Vama Aaah Nawo
Tikayamba zayamba Tikamaliza zathapo, mhu
Sungafewe nthumba mwako usakulimba
Umaona kuwala ukachoka mu m’dima
Phone call ya dollar uku ndikudya limbwa
Ndati eeh “amwene inu mumalima”
Ndichimwana choti chikayaka chimafuna tizilowa Salima
Koma chimakwiya chifukwa ine ndimachikanila
Ati “iwe Spe koma umandifila?” Ndati
Bola ku Likoma Ku Salima nditha kumira
Summertime ndili lake side ndangoika tchingila
Ati body yanga ikuonesa kuti ndayamba ku dhila
Nyimbo zanga tsiku silingaduse osazifila
Ana anamasuka nu hood ghetto tinamangilira
Ndipo sitikusiya
Kuthamanga thamnga N'town kukana kungokhala
Mmutu mwanga mumangoyenda Hustle
Mwana kuthana naye pompo pompo azivaya
Ndilibe Nthawi yama Cuddles
Vama Love sindikupanga nawo
Bola dollar zanga kumazipanga Double
Vama Hate sindikupanga Nawo
Nde ndufuna ukauzane ndi Anzako
Written by: Chifundo Chifundo

Loading...