album cover
Anthem
album cover
Anthem adlı parça {albumName} albümünün bir parçası olarak 265 Records, Madness Ent tarafından 19 Eylül 2023 tarihinde yayınlandıA Quest for Charisma
19 Eylül 2023
Firma265 Records, Madness Ent
DilEnglish
BPM63
Melodiklik
Akustiklik
Valence
Dans Edilebilirlik
Enerji

Müzik Videosu

Müzik Videosu

Şarkı sözleri

Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendele
Gonjetsani adani njala nthenda ndi nsanje Eh
Where you from Malawi!
Pakati ku mpoto ku mmwela?
Where you from Malawi
Mmakonda komwe nnabadwila
Where you from Malawi!
Pakati ku mpoto ku mmwela?
Where you from Malawi
Mmakonda komwe nnabadwila
Ndimakonda komwe nnabadwila
Zakunja sindisilila ndine mtumbuka nde ndimanyadila
Black girls ndimaiifila
Wanyane kweni mulinkhuni eh?
Tikamwe mowa wa nkhuni ehh!
I am from Malawi phala timamwa la Likuni eh
Ndanyamula mbendela mwina dziko ndikusintha ndimmene zinthu zikuyendela
Osapusitsika ambuye amatikondela
Tinjoye tivine gule wankulu "gule wankulu gule wankulu"
Azimayi kuliza nthungululu
Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendele
Gonjetsani adani njala nthenda ndi nsanje
Where you from Malawi!
Pakati ku mpoto ku mmwela?
Where you from Malawi
Mmakonda komwe nnabadwila
Where you from Malawi!
Pakati ku mpoto ku mmwela?
Where you from Malawi
Mmakonda komwe nnabadwila
Ye Chariz!
Dziko la mkaka ndi uchi
Kwabata sungamve mifuti
Timapephela nkachisi Komaso mzikiti
Timalima Chamba timalima tea
Tiyendeleni dindani passport
Panga zotheka utenge permit
Mukhala mwalandilidwa ndekuti eyyy
Timamwa Malawi gin
Ice kuika mchitini
Lake Malawi too clean
Nsomba nasiya kudya za nchitini
Timadya Chambo micheni
Alenje anyamula mipeni
Dzanja linalo chishango
Kumbuyo kuli mikondo
Mulungu dalitsani Malawi musunge mtendele
Gonjetsani adani njala nthenda ndi nsanje
Where you from Malawi!
Pakati ku mpoto ku mmwela?
Where you from Malawi
Mmakonda komwe nnabadwila
Where you from Malawi!
Pakati ku mpoto ku mmwela?
Where you from Malawi
Mmakonda komwe nnabadwila
Written by: Madalitso Kantema, Penjani Malata
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...