Müzik Videosu

Joker (feat. Malinga)
{artistName} adlı sanatçının {trackName} müzik videosunu izle

Şurada:

Krediler

COMPOSITION & LYRICS
Afana Paul Ceez
Afana Paul Ceez
Songwriter

Şarkı sözleri

(Ase Leumas, ma beat bwanji ase?) Tolani Joker Tolani Joker Tolani Joker, Arasi tolani Joker Inu tolani Joker Isssh tolani Joker Tolani Joker, Arasi tolani Joker Tayibakasha Tayibakasha Tayibakasha Eya tayibakasha Eish tayibakasha Tayibakasha Tayibakasha Iwe umatiii! Ndangoponya pick two Support, jump Kuzaponya eight, reverse back Eko ka flower, I want Nyashhh Iwe tatola, knock, cards Aliyense ali ndi Joker wake Aliyense ali ndi Joker wake Aliyense ali ndi Joker wake Aliyense ali ndi Joker wake (Iwe umatii!) Ndangoponya pick two Support, jump Kuzaponya eight, reverse back Iwe eko ka flower, I want Nyashhh Iwe tatola, Knock, Cards Yaa achina Sopano? Reverse, Jump, Knock Bwino pali nthambo za shoko Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko Nda closer knock nkati Tili bho utha Ku checker stat Joker wanga sungamuone ali koyesa dress ya nkwati Ndi woyaka koma alibe smoko Shape ngati botolo la coco Ndi ofewa anakulila ma stocko Ndimamusoka ndekha wona nsoko Ndi wa loyal Joker wangayi Ndi wa local ngati Masayi Ma guy amayesa kumutexta daily hie pansi pa hie Iwe umatii! Ndangoponya pick two Support, jump Kuzaponya eight, reverse back Iwe eko ka flower, I want Nyashhh Iwe tatola, knock, cards Aliyense ali ndi Joker wake Aliyense ali ndi Joker wake Aliyense ali ndi Joker wake Aliyense ali ndi Joker wake Iwe umatii! Ndangoponya pick two Support, jump Kuzaponya eight, reverse back Iwe eko ka flower, I want Nyashhh Iwe tatola, knock, cards Sopano? Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko Nkazi wako ndi njinga mmmh ndawonela ma spoko
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out