album cover
PENSULO
album cover
00:00
00:10
00:15
00:30
00:35
00:40
00:45
01:05
01:10
01:15
01:25
01:35
01:40
02:10
02:50
00:00
02:59
Geçtiğimiz 7 Gün
PENSULO geçen hafta ilk birkaç saniyesinde en sık keşfedilen şarkı oldu

Şarkı sözleri

Nyanda made it
Ooh yeah
Chikondi ndi chipako
Mwini udzakapaka wena
Ine ndili pano, iwe mkumakasaka wena
Ndidzasayinila pensulo, oh
Marriage certificate ndidzasayina pensulo, oh
Kuchitila mwina ukadzasasintha
Pensulo oh
Marriage certificate, ndidzalembapo ndi pensulo, oh
Ma signature tidzafufuta
Mwini yonseyi ni fake loving
Mabodza maningi
Kwachuluka ama pretending
Sindidzafuna oyambana
Adzafunika labala
Ukadzayamba kutamika
Eh, ali ready labala
Ukadzayamba umambala
Pensulo oh
Kuchitila mwina ukadzasintha
Pensulo oh
Signature tidzafufuta
Eh, ukadzayamba dzibelubelu
Kufuna kundipatsa busy
Ukadzayamba dzideludelu
Padzayenda labala, eh
Ukadzayamba kutamatika, eh
Kumafana ndikutamande
Iwe kumadzitama, eh
Padzayenda labala (oh-oh)
Sikuti sindimakukonda, eh
Koma dziko lino lidapenga kale
Anthu ama changer, eh
Ndizasunga labala (oh-oh)
Pensulo oh
Marriage certificate, ndidzalembapo ndi pensulo, oh
Kuchitila mwina (aah-aah)
Adzafunika labala
Ukadzayamba kutamika
Eh, ali ready labala
Ukadzayamba umambala
Pensulo oh
Kuchitila mwina ukadzasintha
Pensulo oh
Signature tidzafufuta
Adzafunika labala
Ukadzayamba kutamika
Eh, ali ready labala
Ukadzayamba umambala
Pensulo oh
Kuchitila mwina ukadzasintha
Pensulo oh
Signature tidzafufuta
Written by: Shaffie Hajj Phiri

Loading...