album cover
GONTHI
album cover
GONTHI adlı parça {albumName} albümünün bir parçası olarak Chifuniro Kasiya, under exclusive publishing license to Newwave Group tarafından 1 Nisan 2026 tarihinde yayınlandıFOREVER AND A DAY - EP
Released1 Nisan 2026
FirmaChifuniro Kasiya, under exclusive publishing license to Newwave Group
DilEnglish
BPM94
Melodiklik
Akustiklik
Valence
Dans Edilebilirlik
Enerji

Müzik Videosu

Müzik Videosu

Şarkı sözleri

Baby girl I gave you a warning
Baby girl I gave you a warning
Baby girl I gave you a warning
Tilipa talking stage, I told you to be patient babe
I knew that I could cause you pain
Koma iwe sunamve (Sunamve)
You thought i can change, ndipo unali ndi confidence (Confidence)
Unkayesa I was going through a phase (Phase)
And now you saying all the boys are the same? (Please stop saying)
Usamanene kuti ndinkakuzunza
Usamanene kuti ndinakuser
Sungandinamizire ndinakuuza (Sungandinamizre ndinakuuza)
Usamanene kuti ndinkakuzunza
Usamanene kuti ndinakuser
Sungandinamizire ndinakuuza (Sungandinamizre)
Ndinakupatsa kale warning
Osagwa nane mu chikondi
Koma vuto lake ndiwe gonthi (Sunganene)
Koma vuto lake ndiwe gonthi (Sunganene)
Ndinakupatsa kale warning (Warning)
Osagwa nane mu chikondi (Kondi)
Koma vuto lake ndiwe gonthi (Sunganene)
Koma vuto lake ndiwe gonthi, yeah (Gonthi yeah)
Oh (Baby girl I gave you a warning)
Gave you a warning (Girl i gave you a warning)
Oh, Oh, hii, mmh
You told me I'm the one you want
Unandiuza that I am your type
Mmh, when you tell me you miss me, falling in love with you was easy, Oh
We can fix this, maybe you're just not in the mood
Ndipange chani baby, do you need some time?
Usamanene kuti ndinkakuzunza (Oh)
Usamanene kuti ndinakuser
Sungandinamizire ndinakuuza (Sungandinamizire kuti ndinakuzunza iwe)
Usamanene kuti ndinkakuzunza
Usamanene kuti ndinakuser
Sungandinamizire ndinakuuza (Sunganame)
Ndinakupatsa kale warning (Warning)
Osagwa nane mu chikondi (Chikondi)
Koma vuto lake ndiwe gonthi
Koma vuto lake ndiwe gonthi, yeah
Ndinakupatsa kale warning (Warning)
Osagwa nane mu chikondi (Chikondi)
Koma vuto lake ndiwe gonthi
Koma vuto lake ndiwe gonthi, yeah
Sindingananene kuti unandizunza (No)
Sindinganame kuti unandiuser
Singandinamizire unandiuza (Baby)
Sindingananene kuti unandizunza (No)
Sindinganame kuti unandiuser
Singandinamizire unandiuza
Falling like a deer
Falling like a deer
Warning
Chikondi
Written by: Chifuniro Kasiya, Daniel Chokhotho, Tunosiwe Mwakalinga
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...