album cover
Moyo
album cover
Moyo adlı parça {albumName} albümünün bir parçası olarak Malawi Goodlife tarafından 30 Nisan 2013 tarihinde yayınlandıUnity
AlbümUnity
30 Nisan 2013
FirmaMalawi Goodlife
DilAlmanca
BPM
Melodiklik
Akustiklik
Valence
Dans Edilebilirlik
Enerji

Müzik Videosu

Müzik Videosu

Şarkı sözleri

Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Ka malata kake tichita kuvitika
Tiyang'ane pambali
Tidzapeza wina akuvutika kopesera ifeyo
Tukudandaula tatopa ndi nyemba
Wina akudya kholowa
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Wina akudwala matenda oopsa
Koma osavuta wanthu
Wina wangopunthwa kachala pang'ono
Akugona mkumabuwula
Poti moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Tizingothokoza pa zomwe tapata
Poti ena alibe
Wina akulira, akufuna nsapato
Wina alibe phazi
Tsiku lililonse kukupatsa moni
Tili bwino pang'ono
Kodi tsono ndi liti mudzayamike Mbuye Mulungu
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Pa dziko lapansi moyo wathu
Timakhumbira zambiri
Tikakhala ndi njinga yopalasa
Ukhumbira ya moto
Ukakhala nayo ya moto udzafunaso galimoto
Koma chodziwika padziko pano
Palibetu kudziwa
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Moyo ndi ovuta
Tikamalalatako inu chikhwaya yang'anani kumbali
Mukapeza wina olemera ngoposa koma wa ulemu
Ngati mukunjoya mudzinjoya mobisira amphawi
Ngati mukuvutika musalembe nkhope mukuvutika
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
Moyo, moyo moyo
Bola osawusanza
Moyo, moyo ndi ovuta
(Moyo, moyo moyo)
Written by: Lucius Banda
instagramSharePathic_arrow_out􀆄 copy􀐅􀋲

Loading...